Reformed Church In Zambia Ebenezer Chainda Congregation

Reformed Church In Zambia Ebenezer Chainda Congregation

Share

30/01/2026

Good morning brethren
The burial for the late Ms. Ngoma Christine will be on Monday 02/02/2026. For more infor can call the church secretary on 0973307182

28/01/2026

Hymn 61πŸ€ŒπŸ‘ŒπŸΌπŸŽ―
1 Konda dzinalo la Yesu
Mwana wosauka 'we;
Ndilo lothandiza anthu;
Khala nalo ponse phee!

Dzina la Yesuyo
Nlokondwetsa onsewo,
M'mwambamo ponsepo
Litonthoza m'mtimamo.

2 Konda dzinalo la Yesu
M'moyo mwako monsemo;
M'mene ulikuyesedwa,
Tchula Dzina lakelo.

3 Dzina ili ndi lokoma
La Mtetezi wathuyo;
M'mene adzatilandira
M'mwamba, tidzakondwadi.

4 Mbuye Yesu timtamanda
Ndi zinyimbo zathuzo;
Mfumu ya mafumu onse
Yesu timayesadi.

11/01/2026
Want your place of worship to be the top-listed Place Of Worship in Lusaka?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Telephone

Address


Lusaka