Anemed Community Based Organization. -Acobo

Anemed Community Based Organization. -Acobo

Share

The organization’s background can be traced from 2016 when a group of determined young people came together with the aim of coming up with solutions to the challenges faced by the community with a biased focus on young people, women, girls and children. ACOBO’s main focus areas include Education, health and economic empowerment, targeting children, adolescent girls and young women (AGYW) and the y

05/01/2026

TIDZIWITSE MAKOLO ONSE , KUTI SUKULU TATSEGULIRA LERO, NDIPO ANA AMENE AKWANITSA DZAKA ZOYAMBA NKOMBA PHALA, ABWERE MALO ALIPO NDITHU. TIPEZENI PA 9 MILES, KUSELI KWA CHIGAYO CHA NGALU (NZERU ZA ANGANGA MAIZE MILL)

maphunziro ndi tsogolo la mwana wathu

06/10/2025

ife a ANEMED CBO, tili achisoni pa za imfa ya yemwe anali mmodzi mwa aziphunzitsi a ku nursery yathu mu czaka zapitazi, uthenga wa maliro watipeza lero madzulo omwe ano. ife tonse pamodzi ndi executive yathu , tili odzadzidwa ndi chisoni ndi imfayi.

mzimu wawo sister Mary Tambala uwutse muntendere.

25/07/2025

Dzulo ndi tsiku lomwe sukulu yathu ya nkomba phala yatsekera maphunziro.

Ndipo panali ana 93, ambiri akukayamba primary. Tithokoze makolo onse omwe munatikhulupilira kubweretsa ana.

Registration iyambika mwezi wa mmawa.

Bwerani ndi ana anu, nawonso alandire maphunziro ankomva phala

26/06/2025

Dzulo talandila mbale zodyera ana, mbalezi zitithandiza kuchepetsa vuto la mbale zomwe zimatichepera kamba ka kuchuluka kwa ana.

Tithokoze a MP athu a zomba likangala mayi ABGAIL BONGWE potipatsa thandizoli.

Amayi pitilizani ntchito zachifundo mmachitazi, tipemphenso kuti ngati nkotheka FIKIRANI ma cbo ambiri omwe ali ndi chidwi chophunzitsa ana a nkomba phala.

Ulemu wanu AMAYI

Want your organization to be the top-listed Non Profit Organization in Zomba?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Telephone

Website

Address


Jali/Phalombe Road
Zomba

Opening Hours

Monday 08:00 - 17:00
Tuesday 08:00 - 17:00
Wednesday 08:00 - 17:00
Thursday 08:00 - 17:00
Friday 08:00 - 17:00
Saturday 08:00 - 12:00