DALI BEATS
14/03/2026
GOOD NEWS!
Kuyambira lero mpaka mtsogolomu, you will now be able to stream and download my free instrumentals on your favorite website
Enjoy! 😍
https://share.malawisongs.com/song/2OqioHnYFvyU?UI=share&SrcWeb=malawisongs
10/01/2026
Inu mwaziwapo ndani apa?🤣🤣
07/01/2026
GOOD MORNING! TABELEDWA IFE😔😭
Aliyense amene analowa m’nyumba mwanga ndi kuba ndalama, ma phone awiri (Smartphones), zovala, laptop ndi desktop yomwe ndimapangila za studio, munaiwala foni yanu pa tebulo.
Ndikudziwa kuti ndinu ndani, ndinalowa pa Facebook yanu ndipo ndaona nkhope yanu.
Muli ndi 24hrs yokha kuti mubweze katundu yense komanso mukonze chitseko. Mukalephera, ndidzachita zomwe ziyenera kuchitika ine za police sindipanga nawo
Account ya Facebook yanu yasiyidwa pano kuti aliyense adziwe
👇👇
https://www.facebook.com/profile.php
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the public figure
Website
Address
Zomba