Sports desk

Sports desk

Share

28/10/2025

Timu ya mikango yofiira kuzomba yomwe ndi yachisilikari Red Lions ikuchita bwino kwambiri mu ligiyi

pakadali pano red lions ikutsogola ndi mapoints 36 pamene yasewera masewero okwana 16

pambuyo pake pakubwera Baka City yomwe ili ndi 29 points pama gamu 16

Sports desk

14/04/2021

-resultS
Pa 14 April 2021

Mighty Wanderers 4-1 Ntopwa
Babatunde Hendlix
Wadabwa
Sanudi
Kaliat

05/04/2021

YA FIFA WORLD CUP 2022 QUALIFIERS

Bungwe la mpira wa miyendo pa dziko lonse lapansi FIFA latulutsa ma fixtures ammagulu

Ndipo team ya dzikolino ya flames ili gulu(D) ndi mateam monga Mozambique, Cameroon ndi ena ambiriii

Want your business to be the top-listed Gym/sports Facility in Zomba?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Telephone

Website

Address


Chikwawa
Zomba