KlickInk
Ndimacheza naye
Ndi mesho wa ine
Koma kumbali afuna azizembera nkazi waine
Ndimadekha naye
Kumasuka naye
But mwatenga stage
Kuti zikomere iyee
Pachigulugulu kundipopa
Kumbali akundikoka
Kuti ndigwere pansi
Kenako azindiseka
Eeeeh
Lyrics
Np 2Face
https://www.facebook.com/1476500332562684/posts/3091690454376989/
Kwacha kwacha
Samalani ndi ma 2face kunjaku
28/01/2022
nyimbo zabwino
Klick Ink - 2Face (M2-Cool x Redemption) Prod. King Duda - Malawi-Music.com Check out 2Face (M2-Cool x Redemption) Prod. King Duda by Klick Ink. This 02:55 Dancehall from Malawi's #1 source of entertainment malawi-music.com.
13/01/2022
https://www.facebook.com/109434657187446/posts/468311027966472/?app=fbl
Ku karonga kumachoka anthu otha kuyimba🙌 listen to this tune🔥 mundiuza.. M2-cool ft Redemption_ 2Face
Hook
Usamuone kusekelera choncho/
alibe umunthu akuputira nkhondo/
samala naye akuponyela nkondo/
manah him ah pagan akukankhila dungeon/
ali ndi mpeni ku mphasa yeeee yeee/
canal mind inangodzadza yeee yeee/
nuff ah dem dem ah 2Face 2face safuna kuona your progress
X 2
https://mikozinet.com/m2-cool-x-redemption-2face/
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the business
Telephone
Website
Address
Mzuzu