Merlam

Merlam

Share

10/07/2026

Anthu inu mwachimwa poganiza koma mukudziwa? ๐Ÿ˜ซ๐Ÿ˜‚

Post ija ndinkatanthauza kuti Charisma amakonda kudya ma orange, osati zomwe munkaganiza zija. ๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚๐Ÿ˜‚

Anyway ๐Ÿฅณ, zikomo kwambiri chifukwa cha support yanu. Video yathu ya "Pena" yakwanitsa 100k+ views pa YouTube.โค๏ธ๐Ÿ™๐Ÿพ

02/07/2026

Ku video shoot Kumakhala zinthu๐Ÿคฃ๐Ÿ˜‚๐Ÿ™Œ

https://youtu.be/yV5w8Z8A_ZE?si=mr6vvcP1I1qVg3Sv

Want your public figure to be the top-listed Public Figure in Mzuzu?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address


Mzuzu