Funcity

Funcity

Share

Enjoy a day of fun, games, and fitness activities while creating unforgettable memories together. πŸ“ Area 10, Lilongwe, opp. Playground, Birthday Parties, Gamestreet, Sweet Shop, Restaurant and much more!

25/12/2025

Ho ho happy holidays! πŸŽ…πŸŽ„ From all of us at FunCity, may your Christmas be merry, bright, and full of laughter, joy, and magical memories.

08/12/2025

Tikupereka ma Ticket mwaulere πŸŽ„πŸ₯³

Mukufuna kuzasangalala Kwa masiku onse awiri a Christmas Market mwaulere? πŸ€—

Satilani ndondomekozi kuti mukhale ndi mwayi opambaba Ticket ya ulere

πŸ‘‰πŸΎ 1. Pangani Like post yathuyi kuti mulowe nawo mmayere otsatira.
πŸ‘‰πŸΎ 2. Pangani tag anzanu okwanira atatu (3) amene muzabwere nawo Ku Christmas Market
πŸ‘‰πŸΎ 3. Lembani comment yanu yofotokoza chifukwa chomwe Mukufuna kupambana ticketiyi
πŸ‘‰πŸΎ 4. Tsatilani tsamba lathu la nchezo (Facebook) kuti mudziwe yemwe wachita mphumi.

Comment yomwe izakhale ndi ma likes ambiri komanso kutsatila malamulo onse azapambana.

Tiyeni nazoniiii πŸ₯³πŸ₯³

Want your establishment to be the top-listed Arts & Entertainment in Lilongwe?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Website

Address


Area 10
Lilongwe

Opening Hours

Monday 08:30 - 16:30
Tuesday 08:30 - 16:30
Wednesday 08:30 - 16:30
Thursday 08:30 - 16:30
Friday 08:30 - 16:30
Saturday 08:00 - 18:00
Sunday 08:00 - 18:00