YOUTH ALERT

YOUTH ALERT

Share

we air on
Mzati FM (Mondays 4pm - 4:30pm)
YONECO (Wednesdays 4:30pm - 5pm)
ZBS & Chirundu FM (Fridays 4:30pm - 5:00m) This page is sponsored by Family Health Services (FHS) with funding from the German Development Bank through KFW; the UK government through Foreign and Commonwealth Development Office (FCDO). Views expressed in posts and comments on this page do not reflect the comments and views of the donors.

28/04/2026

Madolo,

“It’s just a comment… or is it?” 💻🔥

What starts as a joke in the comments can turn into real damage.
Cyberbullying is louder than we think—and closer than we admit.

👀 Have you ever been targeted… or stayed quiet while it happened?

🔥 Full episode dropping soon

21/04/2026

Happy World Creativity and Innovation Day! 🎨✨

Lero pa World Creativity and Innovation Day tikukumbutsa tokha kuti creativity si ya ma artist okha ayi — aliyense ali ndi mphamvu yopanga ma ideas atsopano. Kaya ndi pa hustle yanu, bizinesi, sukulu kapena pa moyo watsiku ndi tsiku — thinking differently is power.

Nthawi zina timaganiza kuti “zilipo kale,” koma innovation imayambira pa ma small ideas amene timanyalanyaza. Maybe idea yanu ingasinthe community yanu kapena ngakhale dziko lonse 🌍

👉 Call to action:
Tell us in the comments — ndi idea yanji yomwe muli nayo koma simunayambe kugwira ntchito nayo? kapena what’s one creative thing you’ve done recently?

Let’s inspire each other 💡

17/04/2026

Happy new weekend! 🍻🔥
Kodi ma weekend timasangalala kapena tikungotha ndalama chifukwa cha pressure ya anzathu? 🤔
Friday kufika… ma plans ayamba: bar, bottles, ma ‘baes’…
Monday kufika… ndalama zatha, ma stress ayamba 😅
Kodi tikusangalala zenizeni kapena tikungotsatira hype? Comment below 👇🔥

Want your business to be the top-listed Business in Lilongwe?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Telephone

Address


Family Health Services (FHS)/
Lilongwe