ICheck
29/06/2023
Osazitengeratu. Sizoonayi!
26/06/2023
Coming up later this week, the Malawi Communications Regulatory Authority (MACRA) will be hosting an important event in Lilongwe. The communications regulator will bring together social media influencers from across the country. The purpose of the event is to educate them on the laws governing social media spaces, as well as discussing issues such as fake news and cyberbullying. This is an important meeting and we look forward to keep you informed on the proceedings!
19/06/2023
Samalani ndi akathyali - Airtel Yachenjeza!
Kampani ya Airtel Malawi yachenjeza kuti pali akuba ena omwe akufuna kubera anthu pofalitsa mipikisano yachinyengo.
Akubawa akumaika zizindikiro ndi makaka a kampaniyi pamauthenga achinyengo omwe akumafalitsawa.
Chitani izi pofuna kuziteteza kwa achinyengo otere:
1. Musayerekeze kulowa mumpikisano uliwonse musanatsimikize kuti omwe akonza mpikisanowo ndi a kampani yomwe akuti yakonzayo. Chitani izi poyang'ana pa masamba a Facebook, Twitter kapena pa website yawo. Komanso, mverani wailesi chifukwa mipikisano yotereyi amaifalitsanso pa wailesi.
2. Musapereke SIM card, chaunzika kapena zomwe zili pa chitupa chaunzikacho komanso numbala yanu yachinsinsi.
3. Ngati mukafunsidwa kuti mupereke zinthu izi, dziwani kuti ndiakuba. Adziwitseni apolisi komanso a Airtel kuti athane ndi akubawo.
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the business
Telephone
Website
Address
Area 49
Lilongwe