Mjidi multimedia
Amangidwa ataba khanda
Apolisi mboma lamangochi akusunga mchitokosi mai wazaka 22 kamba koba mwana wamzake wamwezi umodzi pasiku apitawa. Mzimayiyu ndi alucia saidi.
Pakanali pano khandali lilibwino ndipo labwezeledwa kwamai ake alatina wisiki azaka zakubadwa makumi atatu ndi anayi.
Poyankhula ndi mneneli waapolisi mmboma lamangochi a amina daudi ati mayi wakubayu wakhala akuyesela k*t apezemwanawakewake koma sanakwanitse kupeza mwana ndipo anaganiza zakuba mwana wamzakeyo ndikunamiza abale ake k*t wakamutenga kunyumba yamcherezo k*t adzimusunga kamba koti mayi wake wamwanayo anamwalila akubeleka.
Xhaka scores a third goal at 71 minutes
Arsenal 3-1 manchester united
Ndine okhutila ndimomwe mbewu zikuchitila mchaka chino.
Mtsogoleli wadziko lino wati ndiokhutila ndimomwe mbewu zikuchitila chaka chino. A chakwela alankhula izi atamaliza kuendela mbewu mboma la ntcheu mfumu yaikulu njolomole.
Mmau awo ati izi zathandiza k*t amvekuchokela kwaini ake alimi pazamavuto omwe akukumana nawo and iwo ati awalimbikitsa alimi omwe mbewu zawo zikuchita bwino k*t apitilize kusamalila mbewuzo k*t adzapeze phindu lochuluka.
Iwo atiso mukuona kwawo chaka chinu mbewu zikhoza kuchita bwino ndipo ati sawaiwala mabanja omwe zinthu zawo sizikuyenda bwino mundondomeko yothandiza mawanja ovitika.
Mnkhala pampando wachipani cha MCP mchigawo chapakati , patrick chilondola waikila kumboyo mtsogoleli wadziko lino Dr chakwela k*ti pomwe amkalowa mboma anapeza zinthu zitaonongeka kwambir kotelo iwo akuesetsa kubwezeletsa ndikukomza zinthu zomwe zinaonongekazo.
Malingana ndachilondola ati msonkhano wachitukukowu wawabweletsa pamodzi anthu azipani zosiyanasiyana ndipo izi zaonetsa k*tsutsana ndimagamizo omwe anthu anali nawo oti mu mgwilizano wa Tonse muli kugawanikana. Iwo alankhula izi pamsonkhano wachitukuko omwe wachitika ku ntcheu mu dela lamfumu yaikulu makwangwala.
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the business
Telephone
Website
Address
Kachere
Lilongwe