Spack Debt Collection Agency

Spack Debt Collection Agency

Share

24/02/2026

WANGONGOLE OSAMULODZA AYI!

Ali ndi ndalama zako zambiri nde umulodze akafa iwenso waluza ndalama zako nde wapindula chani?

Osavutika nazo zimenezo, tangobwerani ku Spack Debt Collection Agency tikatenga ndalama zimenezo.

-Mwina poti ndi mzanu kwambiri
-Kapenatu ndi wachibwenzi
-Kapena anangokuberani
-Kapena sakupereka ya rent kwa nthawi yaitali
-kapena njira zambiri zomwe zikukukanikitsani kuti mutenge ndalama zanu? YANKHO MWALIPEZA:

SPACK DEBT COLLECTION AGENCY YAFIKA KWA INU KUTI MUTENGENSO NDALAMA ZANU:

Spack debt collection agency ndi akadaulo omwe amabwerapo mukakhala kuti mwavutika ndipo iwo amakutengerani ndalama zanu mu njira zabwinobwino.

Tawayeseni lero powapeza kwa Chinsapo 1 pa Manda Stage kapena ku branch yawo ku Area 3 ku Lilongwe. Tawapangeni WhatsApp kapena kuimba kumene pa 0880 985 555 kapena 0999 220 720.

24/02/2026

Hello.

Tabweratu chaka chino tikatenge ngongole zanu zija. Titumeni.

Photos from Spack Debt Collection Agency's post 20/10/2025

PREDICT AND WIN

Muli ndi ufulu ndithu woganiza bwino kuti Kodi nkutani koma loserani molondola masewero a timu ya FCB Nyasa Big Bullets komanso Mighty Wanderers omwe aliko lamulungu likudzali.

Anthu asanu adzalandira K2,000 aliyense kuti inuyo mumve kukoma.

Tikunena kuti ngati muli ndi munthu yemwe akukana kukubwenzerani ngongole yomwe anatenga kwa inu, tiuzeni ifeyo zimenezo tikatenga.

Yekha yemwe amatsatira tsamba lino komanso wapanga share ali ndi mwayi opeza kangachepeka.

Idzatsekedwa lamulungu nthawi ya 13:00hrs.

Want your business to be the top-listed Finance Company in Lilongwe?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Telephone

Website

Address


Lilongwe