ICBM DAWAH CLUB
Ukamagawa uthenga wa choonadi kwa anthu ofooka chikhulupiliro amakuyankha👇👇
"Lalikiran zoyanjanitsa osat k*tigawanitsa"
Kod munamba mwalingalirako k*t inu ndamene mumatigawanitsa potuluka mwaife?
Ndithu sali mwaife amene angabwere nd chopeka Bidia
Funso
Munthu akufuna kupanga banja(sex) mu nthawi ya Swaum ndye wamasula kae kenako kupanga, Kod nae akuenera (kuzasala 60days)
Answer
Yes azabweze tsikulo and 60days كفارة chifukwa wapanga exposure Haram ya mwez wu
أراد أن يجامع في رمضان، فأكل قبل الجماع هل عليه كفارة؟؟
يجب كفارة لأنه هتك حرمة شهر
(الجمهور)
(جامع العام الأحكام صيام، ص ٢١٧)
Kodi mwalonjezedwa k*t mawa mulifika?
Let's Change its not too late
May Allah bless you All!!
Milaad Nabiyy???
Kukubukira kubadwa kwa mtumik palibe dipo Lili lonse kupatula moto
كل محدثة بدعة و كل بدعة في النار
Ndipo izi zosangalala nd Zina mwa zopeka mchipembedzo
وعليكم بسنتي و سنة خلفاء الراشدين umenewo Nd Umboni okwanira kwa amene Allah wamuonesa chiongoko
Mwiniwake Ali moyo sadapange makhalifa sadapange ma tabiu sadapange ma tabiu tabieena sadapange... Who are u?? Umboni ndapereka wo Nd mau ochokera kwa mtumik k*t *tsatilan ine komanso MA Khalifa* nde onsewo sadapange inu mutsatira ndan???
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Telephone
Website
Address
Blantyre