Associate Steel Engineering

Associate Steel Engineering

Share

05/10/2024
08/08/2024

Kod mwadziwa? Podziwa mene dzikoli likuyendera, a Associate Steel Engineering, abweresa promotion ndipo Product or service iliyonse yasika mtengo ndi 5% pa mtengo wakale ndipo transport ndiyogawanabe kwa inu akutali ndipo Blantyre, Chiradzulu ndi free delivery. Call or sms 0994337829 & 0885882675 ndipo Whatsapp 0988474880. Promotion ikutha pa 30 September.
Terms and conditions apply

28/04/2024

Wawa ma customers, ndiganiza muli bwino nonse.

Kod mukusaka amisiri ozapanga denga lanu lazisulo, ma gate, ziseko, mawindo, machine owumbira njerwa, kuboola, mipanda, ma protector, ma trailer a galimoto,, kusintha lorry kukhala yonyamulira ziweto, stand ya tank ya madzi, machine opangira chiponde, popcorn machine, zigayo, steel maintainace, piping, interiors, steel furniture ndi zina zambiri?? Musavutike, tipedzeni ife a ASSOCIATE STEEL ENGINEERING mu Blantyre ndipo timapita or kutumiza katundu kulikonse.

Timapangaso fabrication and welding consultation, timapangaso supply services, kuphunzisaso anthu ntchito.

Tiyimbireni pa 0885882675 or 0994337829 ndipo wap 0988474880 or send an email [email protected]

Want your business to be the top-listed Home Improvement Business in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Telephone

Address


Limbe-Mulanje
Blantyre

Opening Hours

Monday 07:30 - 16:30
Tuesday 07:30 - 16:30
Wednesday 07:30 - 16:30
Thursday 07:30 - 16:30
Friday 07:30 - 16:00
Sunday 07:30 - 16:00