Angoni Roots and Culture

Angoni Roots and Culture

Share

23/01/2021

Mchifukwa chanji pamafuko onse mdziko lino la Malawi mtundu wa Angoni okha sudziwika ndi chilankhuro

16/12/2020

u: *MBIRI YA ANGONI A MASEKO.*
Wolemba;George Filiyamu.
_Angoni Roots and Culture_
*Ngwana Maseko*
Ngwana Maseko adali mkulu Wa a ngoni omwe limana lawo lidali kutchedwa kuti Swazi.Iye adali
kutumikira anthu ake pansi pa mphavu ndi ulamuliro Wa *Nxaba*.
Nxaba adali mkulu wankhondo yemwe adatenga nawo gawo yolimbana ndi ulamuliro Wa mfumu Shaka
Zulu mu zaka za 1787-1828.
Ulamuliro ndi ntchito za Ngwana zidali kupereka chiopsezo kwa mfumu Shaka ndipo iye adakonza
Chiwembu chokamuthira nkhondo.
Muchaka cha 1828 Ngwana Maseko ndi gulu lake adachoka mu dziko la *Swaziland* ndipo mu chaka
cha 1841 adamwalira asadaoloke mtsinje Wa _Zambezi_
*Magdlena* adagwirizira ufumu Wa Ngwana ndipo *Mgoola* ndi yemwe adatsogolera gulu la Angoni
kufika Ku Malawi mu chaka cha 1942.

Want your establishment to be the top-listed Arts & Entertainment in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Website

Address


Blantyre