Mussa Adam
11/02/2023
Ma phunziro awulere anzanu akupindula ,timanena mobwereza bwereza kuti mwayi wamaphunziro ukapezeka kumaphunzira zenizeni mpaka umburi wo udzipsa mtima zeni zeni....
Palibe chomwe munthu chingamuthandize moyo uno komanso omwe uli mkudza kuposa kulimbikira kuphunzira deen ndikugwiritsa ntchito zomwe waphunzira zo
Amene tili ndikhombo lofuna kuwonjesera knowledge tiyeni tizisakasaka ma phunziro wo basi deen iyi timayenera kuphunzira daily osazimva kuzindikira kwambiri mpaka kusiya kuphunzira, chifukwa ena ake amakutchani sheikh kapena muft ndi zopanda pake zisakuchedwetseni aliyense ali ndi kuperewera mmaphunziro ake lets work hard pamaphunziro a deen...
Palibe kuthetsa umburi , Bid'ah,shirk popanda kuphunzira deen yi moyenera .....zigawenga zoopseza ndi Bid'ah zili paliponse zikufwambani deen yanuyo ngati muperewere mmaphunziro anu...
Tipemphe Allah atipatse maphunziro opindulitsa ,natipindulitsa muzomwe taphunzira...
Ofuna kuchita join class imeneyi pali timayeso tophweka toti alembe mkulowa nawo mkalasi, zimangofuna wachidwi basi chofuna kuphunzira...
Link yake pansipa
https://chat.whatsapp.com/EzSa5kJVYrKElKVg3EhMSw
16/01/2023
Wife material is the one who is of good character and has good manners. She is not known for foul speech, meanness or bad manners; rather she is good-natured, pure of soul and clean of heart, speaks in a gentle manner and treats people kindly.More important than all of that, she accepts advice and listens to it attentively and wholeheartedly; she is not one of those who are used to arguing stubbornly and arrogantly.
The best of women is the one who, if she is given she is grateful, and if she is deprived she is patient; you feel happy when you look at her, and she obeys you if you instruct her to do something.
She is the one who upholds her connection to her Lord and always strives to increase her level of faith and piety. She does not omit any obligatory duty, and she is keen to do some nafl (supererogatory) deeds. She gives precedence to pleasing Allah..
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Website
Address
Cairo