Frasamiez
Entrepreneur | Content Creator
Business • Motivation • Funny moments
Learn, laugh & grow 🚀😄
Strength for your mind
Peace for your soul 🙏
Follow the page & stay uplifted ✨
25/04/2026
hun sindingapite pa ATM to withdraw money i have flat tyre .
chaii na mi go easy wo 🤣
12/01/2026
Ma big brands monga Nike, Walmart, Abercrombie & Fitch ndi ena akuti Trump’s tariffs akuwakakamiza kukweza mitengo ya zinthu.
Tariffs awa akukweza mtengo wa importing, so makasitomala ndi amene akumva ululu pa prices.
Zovala, ma shoes ndi daily products zikuyembekezeka kukwera mtengo.
💬 Politics ikukhudza wallet ya anthu wamba.
Kukubweraku Trump angoonongapo zithu awa
10/01/2026
🇺🇸🔥 BREAKING NEWS | Syria
US limodzi ndi partner forces achita large-scale airstrikes ku Syria, kulimbana ndi ISIS targets, malinga ndi US Central Command (CENTCOM).
Ziwawazi zidayambitsidwa pa lamulo la President Donald Trump loweruka, ngati gawo la Operation Hawkeye Strike, kubwezera attack ya ISIS yomwe inapha asilikali a US ku Syria pa 13 December.
CENTCOM yati izi zachitika pofuna kulimbana ndi terrorism komanso kuteteza US ndi partner forces m’dera limenelo.
🗣️ CENTCOM message ndi yolimba:
“If you harm our warfighters, we will find you and kill you anywhere in the world, no matter how hard you try to evade justice.”
Uthenga wake ndi umodzi: US siyikusewera—anyone akakhudza asilikali awo, adzayankhidwa mwamphamvu, kulikonse padziko lapansi 🌍
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the business
Telephone
Website
Address
SANDTON