Mintchana

Mintchana

Share

Photos from Mintchana's post 22/06/2026

Sad news πŸ’”

Kwachitika ngozi yoopsa truck ya f and f yomwe inatenga katundu wa anthu aku Capetown yaombana ndi bus yomwe imapita ku malawi ,akuyandikira kufika ku malawi

Ndipo anthu awiri omwe anali bus mo amwalira 😒

Kuthawa xenophobia kukamwalira pa ngozi 😒 😭tsoka lanji a bale

Ena kutumiza katundu kuti akafikirepo truck kuchita ngozi 😒 😭

22/06/2026

Zoti kasikatu pano simukunena Koma kakakweraso eti? Ana anjoka πŸ˜­πŸ˜­πŸ˜­πŸ’”πŸ’”πŸ™ŒπŸ™Œ

Long live Mkulukuta Moyo πŸ”₯

21/06/2026

Olo zizivuta kumalimbikiratu kukankha kumeneko Moyo ndi Wezi wezi πŸ™ŒπŸ™Œ

Photos from Mintchana's post 21/06/2026

Mwana olimba ntima amakhala pambali pabambo ake nthawi iliyonseyo ngakhale yolemetsa anali chifupi nawo.

Pepa Kansengwa jnr πŸ’”πŸ’”

21/06/2026

Mwana wa malemu kansengwa wati apitili ntchito yomwe bambo ake amagwila komanso azigwilitsa ntchito ma phone numbers a bambo ake.

Want your public figure to be the top-listed Public Figure in Blantyre?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Website

Address


Blantyre