Qualifies Motha

Qualifies Motha

Share

10/07/2025

Landlords

01/07/2025

The Best wishes for Exams shouldn't delay you working hard.

01/07/2025

All the best to you all who are sitting for Malawi School Certificate of Education. Work Hard, Pray Hard and write neatly. You are the next generation for the leadership and transformation of your area

01/07/2025

Komatu ma game enawa🤣🤣🤣🤣

01/07/2025

Kumasangalalatu kumeneko 🤣🤣

01/07/2025

With Twnda – I just got recognized as one of their top fans!

24/06/2025

Bambo wazaka 73 Lyson William ochokera m'mudzi mwa Chagoma kwa mfumu yaikulu Phalamba m'boma la Ntcheu wamwalira kaamba komwa mowa osadyera.

Mneneli wa polisi ya Ntcheu a Jacob Khembo atiuza kuti bamboyu yemwe banja lake lidatha ndi mkazi wake amakhala yekha ndipo pa 22 June chaka chino anapita kukamwa mowa koma asanadye chakudya chilichonse.

A Khembo ati m'mawa wa pa 23 June abale a bamboyo sadaone bamboyo akutuluka mnyumba ndipo chitseko chidali chotseka zomwe zidawakakamiza kuti athyole chitsekocho.

Atalowa mnyumbamo adapeza bamboyo atamwalira kale ndipo apolisi yaing'ono ya Senzani ndiwo adakatenga namwino pachipatala chachin'gono cha Senzani omwe adapima thupi labamboyo ndi kutsimikiza kuti bamboyo wamwaliradi kaamba komwa mowa osadya.

Kotero apolisi m'bomali apempha anthu kuti apewe kumwa mowa osadya ponena kuti bambo winanso Beyard Kelvin wazaka 33 ochokera m'dera la mfumu yaikulu Njolomole nayenso adamwalira kaamba komwa mowa osadya sabata yathayi.

Wolemba Bertha Banda

24/06/2025
24/06/2025

Hahaha ati creativity 🤣😂

24/06/2025

Nde kunali akulu awa

24/06/2025

Mukuzunzika bwanji anzathu kumeneko🤣?

23/06/2025

Komanso zomati wanditayisa nthawizi nde nzopepera nde kuti iwe umakanika kupanga ma programme ako nkhani ya nanzezeyo? Nde opusa ndiwetu🤣🤣

Want your public figure to be the top-listed Public Figure in Phalombe?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Website

Address

Phalombe