STORY TIME
Iyi ndi page ya nkhani imene mwini wake ndi HUMBLE CEE page iyi ndiyazilembo zikuluzikulu
Wina akhoza kupanga page yake yofanana ngati yangayi ziwani kuti ndi fake page
Timapanga za nkhani basi palibe zina
Zokhumba zanga ndi kupitisa pasogolo luso la nkhani pangani follow page yanga ndikumawelenga nawo nkhani zathu mosavuta ndi mosangalala
21/07/2026
#πΉ *THE WRONG SACRIFICE*βΌοΈπΉ
Chapter 24
Story Done by
LND CHIKUNβοΈFt STEPHANIE
0998242764/0999739805 *Home of Super stories Gp* INCLUDING *ADMIN PANEL STORY GROUP*
ππππππππππππππππππππππ
_MORE COMMENT MORE SHARE MORE_π₯π₯π₯π₯π₯π₯π₯π₯π₯π₯π₯π₯........
π₯Ύπ₯Ύπ₯Ύπ₯Ύπ₯Ύπ₯Ύπ₯Ύπ₯Ύπ₯Ύπ₯Ύπ₯Ύπ₯Ύπ₯Ύπ₯Ύπ₯Ύπ₯Ύπ₯Ύπ₯Ύπ₯Ύ
..nkhope ya clever yidabwera tsinya pang'ono, download atamalizika , clever adayamba kuona zinthunzi zochuluka zomwe zimaonetsa tapiwa ali ndi mnyamata , mpaka video yomutsatira mnyamata , . malaya a clever adayamba kutentha , cholembera chomwe chidali m'manja adachigwetsera pa form yomwe amalembapo , .
adadzuka mkutenga jacket yake yomwe adayikoleka pa mpando mkuvala adatuluka mu office, mkutseka ndi makiyi, phone adayiponyera m'nthumba , sadamuyankhe kalikonse mzake uja pa chilichonse chomwe adalemba ku chat ......
adakakwera galimoto , ndipo nkhope yake yimkaoneka yokwiya kwambiri , adaliza galimoto isadanyamuke yidalira mofuula kenako idanyamuka koma mochita kupalasa matayala am',mbuyo , kusonyeza kuti yidanyamuka mwa mphamvu .........
tikaone kuti kukachitika zotani .....
Apa mkuti tapiwa atafika mtauni akupita kunyumba , atafika mwanthawi zonse adafikira kufunsa mwana wake kuti wamusowa , wantchito adayankha kuti mwana akugona, adalowa mnyumba adapeza mwana atagona pa mpando.
adafikira kumukisa pa tsaya , my baib eshiii miss u , atamaliza kulankhula adapitilira poti mwana adali ndi tulo .
mada adatenga family ya kwawo yonse ulendo wakunyumba , adayamba kudzera ku chilomoni kukasiya aprophet kenako adapita kwawo ku chilimba.
mada koma why tapiwa amapanga ngati si uja amkakunyoza uja ,,,,,,,, sindikudziwa , komano abusa aja anandirankhula kuti ineyo ndimumasukire koma akakamba za ubwenzi pokhapo ndisayerekeze , mwa wayi sadakambe . ,,,,,,,, olo ineyo sindingakondwe kukuonani mukubwelerana achimwene , tapiwa ndi mkazi wa mwano hvy moti sindikufuna mudzabwelere moyo onyozedwanso ndi tapiwa ,,,,,,,,,, kkkkkk sindingabwelere naye ngati akufuna kumangocheza no problem but relationship ayi ayi ndithu .
adafika kunyumba , kutulutsa mphatso zomwe adapatsidwa ndi aprophet kenako adalowa m'nyumba kukakonza chakudya chamadzulo , apa mkuti galimoto ili pa bwalo programme idali yoti abweza mawa .
clever adathamangitsa galimoto from zalewa nde galimoto idathamanga , , adafika kumandala koma horn yomwe idaperekedwa pa Gate eshiiii, . tapiwa palibe chomwe amadziwa , mtima udali pamsi , clever adatsekulilidwa ndi gateman , atangotsekula galimoto lidathamangira pa car park ngati siyima , moti Gate man adangoyima kumuyang'ana asadatseke Gate.
galimoto itapanga Park, clever adatsekula mwachangu chitseko kwinaku akutchula dzina la tapiwa koma chifukwa choti chinyumba chidali chachikulu . tapiwa!!!!!tapiwa!!!! . amayitana kwinaku akuyenda ndawala kutsekula m'nyumba.
wantchito wa mnyumba adatutumuka ndikatsekulidwe kachitseko , adadzidzimuka ataona kuti ndi bwana . adalowa mkufunsa yes where is your madam ,,,,,,,, alikuchipinda , apa mkuti tapiwa akusintha zovara .
atatsekula chitseko chakuchipinda adapereka mbama ya mmakutu asadafunse , phone ili m'manja, tapiwa adagwera pa bedi koma mwendo udamenyeka ku mwendo wa bedi , tapiwa adagwira mwendo mkuno wina ukutikita pomwe adamumenyapo uku akugwetsa msonzi , atangogwa tapiwa adazindikira kuti ndi mamuna wake , eshiiiiiii clever ndi chaninso mayine mwendo wanga eshiiiiii koma ndidzapuma litilo ine mayine ,,,,,,,,,check on this phone , uyu ndindani uyu sishupiti ,,,,,,,,, clever ukanandifunsa bwino bwino nde ndifotokoze , u mean ndani mamuna yemwe angasekelere izi ,,,,,,,,,, clever sizomwe ukuganizazo pls ndisiye ndifotokoze ,,,,,,,clever adalumpha ndi Kiki yomwe yidamufikira tapiwa m'matako , tapiwa sadapatsidwe mwayi ofotokoza koma kumangolira , tapiwa adalira mokweza , koma poti chipita chawo adatseka komanso celling mawu samamveka kunja . clever sadasiye kumumenya mpha adamupweteka munthiti . tapiwa adalira momvetsa chisoni kwinaku akuoneka ndithupi lotopa , amawoneka wofooka mawunso amatuluka mofooka , clever adasiya kaye kumenya kuwopa zapadzana .
tapiwa adayamba kumuganizira kwambiri mada , eshiiiii uyu adzandipha ndithu , tsiku lina ndidzatsatira makolo anga chifukwa cha nkhanza za mkuluyu eshiiiii , mpaka mwana adadzuka mkuyamba kulira . maganizo wothawa adamupeza , clever adatuluka mnyumba mtima uli wawu kali thukuta likutuluka , wantchito sadadziwe kuti chikuchitika , amayika chakudya pa tebulo , wantchito sadamve mfuwu uliwonse koma amangoona momwe amaonekera abwana amuna kuti zinthu sizili bwino , grace adawauza abwana kuti chakudya chatheka , clever adangovomera ndimutu , kenako grace adapita kuma cottazi kwake kukakonza za chakudya chake . clever amadzimva kukhuta komanso appetite adalibe , adakhala pa mpando tambula la madzi lili m'manja .
tapiwa adali akulira kwinaku akugwira mwendo wake komanso tsaya lomwe adamenya lidayamba kutupa , amadzifunsa kuti wapanga zimenezija ndindani mpaka kufatsa kumawa jambula , eshiiiii koma akadakhala mada sakadafikira kumumenya I think amuna ophunzira ndi odzimva nzeru kulemera , ndisake osaphunzira olo mphunzitsi mwina mkumvako chikondi , koma what about mada my love , my first one who remove my virginity,. my man pls ,my man ndiwe wekha , abusa adanenelerako za yiwe , ndikhululukire mamuna wanga , mada .
nthawi imapita tapiwa akulira kuchipinda clever asadatulukire.
clever maganizo omuchotsa tapiwa kukhala mkaxi wake amabwera ndithu , . apa mmene zikuonekera banja lithe ndizingolimbana ndi azimayi oyenda yenda omwewa kusiyana ndimunthu ondeswera mtima ngati uyu chifukwa tsiku lina adzandigwiritsa murder uyu .
nthawi m'mene imafika 11 usiku aliyense adali asadagone .
kukangocha ine ndithawe ndidzipita chonde kwathu kumudzi kaye eshiiiiiii.
clever adapita kogona koma maganizo adali oti kukacha adzapite kwawo kwa tapiwa akadandaule . usiku umenewu onse adagona osadya komanso osayankhulana , aliyense adagona ndi maganizo .........
next part 25.....
let's share to all groups
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Contact the public figure
Telephone
Website
Address
Ntaja