Kitanna Project
We believe education is key to overcoming poverty, inequality, and social exclusion.
12/06/2025
KODI BUNDLE YATHA ?
Nkutheka mumaphunzira online ndipo bundle yakutherani muli ndi nkhawa kuti sogolo lanu lasokonekera . Ngati mukukhala ku nkhatabay ndi madera odzungulira musadandaule Ku Njaya lodge kuli kitanna project , ndipo cholinga ndi kuonetsetsa kuti aliyese ali ndi kuthekera kotenga nawo gawo pa za tekinology . kumeneku timakupasani WIFI othamanga komaso Maphunziro a ulele a Compyuta Sizidalira kuti mudalekeza pati komasotu zonse ndi za ulele
Nde mukuchedweranji tipezeni lero Ku Njaya lodge lero
Tiimbileni phone lero
16/05/2025
💻 ZONSE ZA ULELE ! Wi-Fi + Kuphunzira Computer Mwa Ulele
Eya Ndi zoonadi — Ndi Kitanna Project zikutheka ,Pofuna Kuti Aliyestse akhale ndi Mwayi Wodziwa Za Tekinoloje
📍 Project ikupezeka ku Njaya Lodge, Nkhata Bay
◾ internet Ya Ulele
◾Maphunziro a Compyuta A Ulele
◾Aliyese atha kubwera !!!!
Kodi Mukufuna Kulowa Nawo mu project Imeneyi ?
📞 Tiimbileni pa Manambala Omwe Ali Mmsiwa – Ndipo Pamodzi Tikonze tsogolo komaso Masompenya anu pa Tekinoloje . Yankhulani Ndi
Dixon junior : +265 991476780
Lily phiri : +265 980112638
Gilbert mafunga : +265 999948673
10/05/2025
🚀 Nkhatabay Youth – This One’s for YOU!
If you’ve signed up for an online course but don’t know how to begin…
If you want to learn computer skills but can’t afford expensive lessons…
If you just need a place with free internet to get started…
👉 Kitana Project at Njaya Lodge has your back!
✅ Free Wi-Fi
✅ Free Online Education Access
✅ Free Face-to-Face Computer Lessons
No costs. No catch. Just opportunity.
📍 Visit us at Njaya Lodge, Nkhatabay
📞 Call us today to get started!
dixon junior : +265 991476780
lily phiri : +265 980112638
gilbert mafunga : +265 999948673
💬 “The future belongs to those who are connected and informed – be one of them!”
🔗
"Empower Your Future – Join the Kitanna Project!"
📢 Are you aged 15 to 35 and living in Nkhatabay?
The Kitana Project, Is here to open doors for you – absolutely FREE!
🌐 Free Wi-Fi
💻 Free Online Learning Support
🖱️ Free Computer Lessons (face-to-face!)
Whether you're already enrolled in an online course or just getting started, we’re here to help you learn, grow, and thrive.
📍 Find us at Njaya Lodge, Nkhatabay, Malawi
📞 Contact us through the numbers below – and let's build your digital future, together.
dixon junior : +265 991476780
lily phiri : +265 980112638
gilbert mafunga : +265 999948673
🔗
Click here to claim your Sponsored Listing.