Inno Fost
Kaya ndikhala ndi moyo kaya sindikhala ndi moyo sindikuziwa
Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Zimba Sinoy, Maupo Samuel, Madalitso Wokonderedwa Tungama, Gilbert Chapita, Honest Banuwel, Paul Simbeye, Babak John, Stanley Chawinga Mw, Hassan Kassim, Godfrey Paul, Mazey Wizi, Innocent Namakwela
Zinthu zake mmmh apa sizidayende olo pang'ono
kwacha bwanji kumeneko family �
Masana anu akuyenda bwanji kumeneko family
Dzuro ndagula kagalu ka 850k Relo kafa,
Akulu akulu aka kokha ndidya 🙌😂💔
Yesu anagwa ku ndilande
Ndalota nditalemera, ndikuyendera Fortuner, alamuanu akuyendera BMW kuvaya kuchigayo
Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Ramzy Van Kitter Longwe, Boyce Frank Kovie, Agness Paul, Vin Kananji MW, Abubakar Uluma, Shæffèï H Màdêrà, Allih Kannih, Leah Mwakikunga, Trust Joseph, Ruth Heru, Bright Masambo, Maness Aron, Stera Chgamula, Mateyo Milaz, Bickton F Jb Madaliso
zochita izi guys
Anthu mumavina ngati mawa kulibe eeeh
Koma nthu aku kasungu sungawamvese
Click here to claim your Sponsored Listing.
Category
Culinary Team
Attire
Address
Lilongwe