NRC
25/11/2025
Tomorrow bwana President akhala live a podcast malawi kuvukuta National Budget.
Komaso akhala ndi program yomwe akambepo nkhani za chuma. Tiyeni ku page yawo tikaikepo maganizo athu pa zomwe mungafune kumva.
https://www.facebook.com/share/1AHnC9Y6PF/
Tomorrow in the morning we will be shooting With Caswell Mkanda. We will discuss in depth on some economic issues. What would you like to hear in our conversation?
In the evening we will be live on podcast Malawi analysing the mid year budget statement that was presented by Honourable Mwanamvekha. What areas would you like to be tackled?
23/11/2025
Recently takhala tikuona dvuto losowa kwa nyumba za rent.
Izi zili choncho tili ndi Malawi Housing Corporation komaso ma bungwe ena a boma amane amayang'anila ntchito zomangamanga. Kupatula apo tili ndi nyumba ma town a Lilongwe, Blantyre, mzuzu zomwe linamanga ndi boma la Kamuzu ndi Malo ena a boma ndi nzika za dziko lino.
Kodi chifukwa china boma silionetsa chidwi chomanga nyumba zamakono kuti nzika zisamasowe pokhala. Nanga bwanji mu budget yadzulo boma likupeleka mwayi kwa a Malawi othekela amene ali kunja kwa dziko lino kumanga nyumba zamakono ngakhale sanatambasule kuti nyumba zimenezi zipeleka mwayi kwa anthu wamba.
Ife ngati anthu wamba timangosilila tikapita dziko la eni mmene ma boma awo amakondela nzika zawo poonetsetsa kuti zili ndi Malo okhala a abwino. Ifeso ngati nzika ndi udindo wathu kufusa mafunso kwa adindo kuti atithandize. Ku dyeledwa ndalama ndi ma agent ngati sikukukwanani tiyeni tikhale tizisiye chonchi mpaka kale.
President Mahata on Cruise 5. Tiyeni tikaionele ya full ku YouTube https://youtu.be/52gXsUvPVgA?si=BGkButk8iqIPcJCF
12/11/2025
🇲🇼 NRC on PROSPERITY: Building a People’s Economy for All
Malawi is rich in potential, yet our people remain poor. Every day, ordinary Malawians wake up early, work hard, and hope for a better tomorrow, but our systems continue to fail them. NRC believes it’s time to change that story.
PROSPERITY is not just about money, it’s about dignity, fairness, and opportunity for every Malawian. It means creating an economy that works for the people, not just for a few at the top.
Under the banner of Prosperity, NRC envisions:
✅ A People’s Economy that supports local industries, farmers, and entrepreneurs.
✅ Job creation through innovation, technology, and small-scale enterprises.
✅ Fair trade and fair wages so that hard work truly pays.
✅ A corruption-free economy where national resources benefit all, not a few.
✅ Economic decentralization: empowering districts to plan and drive their own development.
We believe Malawi can rise again if we rebuild our economy from the grassroots up. We must invest in our people, our land, and our ideas, not wait for foreign aid to define our destiny.
“Prosperity is when every Malawian can afford a decent life, not just survive it.”
The future belongs to those who dare to think differently. NRC dares to imagine a Prosperous Malawi — for all, by all, and with all.
Click here to claim your Sponsored Listing.