MWHYPE

MWHYPE

Share

07/05/2026

Part 3 👉👉Mayi ndi bambo amabanja awo anali pachibwezi kwazaka 15 kufikila bamboyo atamwalira mwadzidzidzi ali kuzinjoyi

Khani ija yafika ku khoti ndipo mayi uja anatulusidwa pa belo kudikilira siku lamulandu.
Siku lamulandu litafika khamu la anthu linapita ndithu k*t likamve chomwe chapha bambo k*t mwina ndi seke seke😆😆 mankhala kapena amugwira pakhosi😒

Mulandu ukuyamba apolice anali ali pomwepo ngati mboni yaboma kubwelesa zosatila zakuchipatala

Khoti linayimisa munthu wamayi k*ti afotokoze mbali yake ndipo adafotokoza motele ku part 1

Ndipo apolice anayima ngat mboni kupeleka zosatila zakuchipatala kwa oweluza

Oweluza anati bamboyi wapita chifukwa cha Bp kuchokela pakanthawi wakhala akulandila mankhwala a Bp apa inakwela kwambili mwaka nthawi imodzi mwachidule ndi infa ya normal palibe wamuchita chipongwe.

Ndipo mayi uja anawoneka womasuka pantawiyi koma angakhale nkazi komaso akuchimuna anali owoneka okhumudwa.

Angakhale mayiyu amawoneka k*ti wamasuka koma kumbukilani anali pabanja ndipo mamuna wake anali ali ku khoti komweko kumvesela mulandu ndipo pabanja lawo anali ndi ana atatu osiyana mawonekedwe🤣🤣🤣

Kodi mutakhala inu mamuna mungatani mupitiliza banja ndi mayi ameneyu
Nanga anawa munganene k*ti onse ndi anu anthu ndikumva???

Tipasen maganizo anu kwasalaku.

Olemba kuchoka ku and 🙏🙏🙏🙏apangen tag azanu

Want your business to be the top-listed Advertising & Marketing Company in Lilongwe?
Click here to claim your Sponsored Listing.

Category

Telephone

Website

Address

Lilongwe